Yoswa 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma amuna enanu, musangoima chilili. Thamangitsani adani anu ndipo muzipha amene muziwapeza.+ Musawalole kuti akalowe m’mizinda yawo, pakuti Yehova Mulungu wanu wawapereka m’manja mwanu.”+
19 Koma amuna enanu, musangoima chilili. Thamangitsani adani anu ndipo muzipha amene muziwapeza.+ Musawalole kuti akalowe m’mizinda yawo, pakuti Yehova Mulungu wanu wawapereka m’manja mwanu.”+