-
Yoswa 10:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Analanda mzindawo ndipo anapha ndi lupanga anthu amene anali mmenemo ndi m’midzi yake yonse, komanso anapha mfumu yawo. Yoswa anaonetsetsa kuti pasakhale wopulumuka. Anachitira mzindawo zonse zimene anachitira mzinda wa Egiloni. Chotero Yoswa anawononga mzindawo ndi aliyense amene anali mmenemo.+
-