Yoswa 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Alimoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.
18 Anatoti+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Alimoni+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.