Yoswa 24:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Kenako munawoloka Yorodano+ n’kufika ku Yeriko.+ Nzika za ku Yeriko, Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi, ndi Ayebusi anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka m’manja mwanu.+
11 “‘Kenako munawoloka Yorodano+ n’kufika ku Yeriko.+ Nzika za ku Yeriko, Aamori, Aperezi, Akanani, Ahiti, Agirigasi, Ahivi, ndi Ayebusi anayamba kumenyana nanu, koma ine ndinawapereka m’manja mwanu.+