Oweruza 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+
2 Ndiyeno mngelo wa Yehova+ ananyamuka ku Giligala+ kupita ku Bokimu,+ ndipo anati: “Ndinakutulutsani mu Iguputo ndi kukulowetsani m’dziko limene ndinalumbirira makolo anu.+ Komanso ndinakuuzani kuti, ‘Sindidzaphwanya konse pangano langa ndi inu.+