Oweruza 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndidzakokera kwa iwe+ m’chigwa* cha Kisoni,+ Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Yabini,+ pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi gulu lake lonse. Pamenepo ndidzam’pereka m’manja mwako.’”+
7 Ine ndidzakokera kwa iwe+ m’chigwa* cha Kisoni,+ Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Yabini,+ pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi gulu lake lonse. Pamenepo ndidzam’pereka m’manja mwako.’”+