Oweruza 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho Gidiyoni anatenga amuna 10 mwa atumiki ake ndi kuchita zonse zimene Yehova anamuuza.+ Koma chifukwa choopa kwambiri anthu a m’nyumba ya bambo ake ndi anthu a mumzindawo, anachita zimenezi usiku osati masana.+ Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:27 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, ptsa. 16-17
27 Choncho Gidiyoni anatenga amuna 10 mwa atumiki ake ndi kuchita zonse zimene Yehova anamuuza.+ Koma chifukwa choopa kwambiri anthu a m’nyumba ya bambo ake ndi anthu a mumzindawo, anachita zimenezi usiku osati masana.+