Oweruza 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mkazi wa Giliyadi anapitiriza kumuberekera ana aamuna. Anawo atakula, anathamangitsa Yefita ndi kumuuza kuti: “Iwe suyenera kulandira cholowa m’nyumba ya bambo athu,+ chifukwa ndiwe mwana wa mayi wina.” Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, tsa. 6
2 Mkazi wa Giliyadi anapitiriza kumuberekera ana aamuna. Anawo atakula, anathamangitsa Yefita ndi kumuuza kuti: “Iwe suyenera kulandira cholowa m’nyumba ya bambo athu,+ chifukwa ndiwe mwana wa mayi wina.”