Oweruza 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa.+ Atafika kumeneko anaona mwana wake wamkazi akubwera kudzam’chingamira, akuimba maseche ndi kuvina.+ Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.
34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa.+ Atafika kumeneko anaona mwana wake wamkazi akubwera kudzam’chingamira, akuimba maseche ndi kuvina.+ Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.