Oweruza 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+
5 Ndiyeno anthu a m’Gibeya anayamba kundiukira, ndipo usiku anazungulira nyumba imene ndinalimo. Iwo anali kufuna kupha ineyo, koma anagwirira mdzakazi wanga+ mpaka anafa.+