Rute 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pamenepo Rute ananyamuka n’kupita, ndipo anakalowa m’munda wina ndi kuyamba kukunkha m’mbuyo mwa okolola.+ Mwamwayi mundawo unali wa Boazi,+ wa ku banja la Elimeleki.+
3 Pamenepo Rute ananyamuka n’kupita, ndipo anakalowa m’munda wina ndi kuyamba kukunkha m’mbuyo mwa okolola.+ Mwamwayi mundawo unali wa Boazi,+ wa ku banja la Elimeleki.+