Rute 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Naomi, apongozi a Rute, anamuuza kuti: “Mwana wanga, kodi sindiyenera kukupezera mpumulo,+ kuti zikuyendere bwino? Rute Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:1 Tsanzirani, tsa. 44 Nsanja ya Olonda,10/1/2012, tsa. 20
3 Tsopano Naomi, apongozi a Rute, anamuuza kuti: “Mwana wanga, kodi sindiyenera kukupezera mpumulo,+ kuti zikuyendere bwino?