1 Samueli 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Hana sanapite nawo,+ pakuti anali atauza mwamuna wake kuti: “Mwanayu akangosiya kuyamwa,+ ndiyenera kupita naye kuti akaonekere pamaso pa Yehova ndi kukhala kumeneko mpaka kalekale.”*+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:22 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 16
22 Koma Hana sanapite nawo,+ pakuti anali atauza mwamuna wake kuti: “Mwanayu akangosiya kuyamwa,+ ndiyenera kupita naye kuti akaonekere pamaso pa Yehova ndi kukhala kumeneko mpaka kalekale.”*+