19 Mpongozi wake, mkazi wa Pinihasi, anali ndi pakati moti anali pafupi kubereka. Ndiyeno anamva kuti likasa la Mulungu woona lalandidwa ndipo apongozi ake ndi mwamuna wake afa. Zitatero, anawerama n’kuyamba kubereka, chifukwa zowawa za pobereka zinam’fikira mwadzidzidzi.+