1 Samueli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anatumiza likasa la Mulungu woona ku Ekironi.+ Ndiyeno likasa la Mulungu woona litangofika ku Ekironi, anthu a ku Ekironi anayamba kulira, kuti: “Atibweretsera likasa la Mulungu wa Isiraeli kuti atiphe ife tonse!”+
10 Choncho anatumiza likasa la Mulungu woona ku Ekironi.+ Ndiyeno likasa la Mulungu woona litangofika ku Ekironi, anthu a ku Ekironi anayamba kulira, kuti: “Atibweretsera likasa la Mulungu wa Isiraeli kuti atiphe ife tonse!”+