3 Iwo anayankha kuti: “Ngati mukubweza likasa la Mulungu wa Isiraeli, musalibweze osapereka nsembe. Mulimonse mmene zingakhalire, muyenera kupereka nsembe ya kupalamula+ kwa iye. Mukatero mudzachira, ndipo mudzadziwa chifukwa chake sanali kuchotsa dzanja lake pa inu.”