9 Ndiyeno muonetsetse izi: Likasalo likadzalowera njira yopita kwawo, ku Beti-semesi,+ ndiye kuti iye ndi amenedi watichitira choipa chachikuluchi. Koma ngati sililowera kumeneko, tidziwa kuti si dzanja lake limene latikhudza, koma ngozi+ yangotigwera.”