1 Samueli 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno anaika likasa la Yehova m’ngoloyo.+ Anaikamonso bokosi lina lija lokhala ndi mbewa zoyenda modumpha zagolide ndi zifanizo za matenda awo a mudzi.
11 Ndiyeno anaika likasa la Yehova m’ngoloyo.+ Anaikamonso bokosi lina lija lokhala ndi mbewa zoyenda modumpha zagolide ndi zifanizo za matenda awo a mudzi.