1 Samueli 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana anu aakazi idzawatenga kuti akakhale opanga mafuta onunkhira, ophika chakudya ndi opanga mkate.+
13 Ana anu aakazi idzawatenga kuti akakhale opanga mafuta onunkhira, ophika chakudya ndi opanga mkate.+