1 Samueli 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.”
22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.”