1 Samueli 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba m’buku limene analiika pamaso pa Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti aliyense abwerere kwawo.
25 Zitatero, Samueli anauza anthuwo zinthu zimene mfumu iyenera kulandira kwa iwo+ ndipo anazilemba m’buku limene analiika pamaso pa Yehova. Kenako Samueli anauza anthuwo kuti aliyense abwerere kwawo.