1 Samueli 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Motero, Sauli anaitanitsa anthu ku Telayimu+ ndi kuwawerenga. Iye anapeza kuti panali amuna oyenda pansi 200,000 ndiponso amuna a ku Yuda 10,000.+
4 Motero, Sauli anaitanitsa anthu ku Telayimu+ ndi kuwawerenga. Iye anapeza kuti panali amuna oyenda pansi 200,000 ndiponso amuna a ku Yuda 10,000.+