46 Lero Yehova akupereka m’manja mwanga,+ ndipo ndikupha ndi kukudula mutu. Lero ndipereka mitembo ya anthu a m’misasa ya Afilisiti kwa mbalame zam’mlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.+ Anthu onse a padziko lapansi adzadziwa kuti Isiraeli ali ndi Mulungu.+