1 Samueli 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sauli nayenso anali kuona kuti Davide akuchita zinthu mwanzeru,+ moti anali kuchita naye mantha.