1 Samueli 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamapeto pake, Sauli nayenso anapita ku Rama. Atafika pachitsime chachikulu chimene chili ku Seku, anayamba kufunsa kuti: “Kodi Samueli ndi Davide ali kuti?” Poyankha, iwo anati: “Iwo ali ku Nayoti,+ ku Rama.”
22 Pamapeto pake, Sauli nayenso anapita ku Rama. Atafika pachitsime chachikulu chimene chili ku Seku, anayamba kufunsa kuti: “Kodi Samueli ndi Davide ali kuti?” Poyankha, iwo anati: “Iwo ali ku Nayoti,+ ku Rama.”