1 Samueli 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yonatani anamuyankha kuti: “N’zosatheka zimenezo,+ suufa. Bambo anga sangachite chilichonse chachikulu kapena chaching’ono osandiuza ine.+ Ndiye bambo anga angandibisire nkhani imeneyi chifukwa chiyani?+ Sizingachitike zimenezo.”
2 Pamenepo Yonatani anamuyankha kuti: “N’zosatheka zimenezo,+ suufa. Bambo anga sangachite chilichonse chachikulu kapena chaching’ono osandiuza ine.+ Ndiye bambo anga angandibisire nkhani imeneyi chifukwa chiyani?+ Sizingachitike zimenezo.”