21 Ndiyeno ndidzatumiza mtumiki kuti, ‘Pita ukatole miviyo.’ Koma mtumikiyo ndikadzamuuza mawu akuti, ‘Mivi ili kumbali yakutiyakuti, pita ukatole,’ iweyo ukatuluke chifukwa ndiye kuti zinthu zili bwino ndipo palibe chodetsa nkhawa chilichonse. Ndikulumbira pali Yehova, Mulungu wamoyo.+