-
1 Samueli 21:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Davide anafunsa Ahimeleki kuti: “Kodi muli ndi chida chilichonse pano, mkondo kapena lupanga? Inetu sindinatenge lupanga kapena zida zanga, pakuti zimene mfumu yandituma zinali kufunika mofulumira.”
-