1 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+
11 Atafika kumeneko, atumiki a Akisi anayamba kunena kuti: “Kodi ameneyu si Davide+ mfumu ya dziko? Suja ankamuimbira nyimbo molandizana mawu, akuvina+ n’kumati,‘Sauli wakantha adani ake masauzande,Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi’?”+