1 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+
23 Patapita nthawi, kunabwera anthu amene anauza Davide kuti: “Afilisiti akuthira nkhondo mzinda wa Keila,+ ndipo akufunkha zokolola zimene zili pamalo opunthira mbewu.”+