1 Samueli 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chonde pitani, mukayesetsebe kufufuza kwa aliyense amene anamuonayo, ndipo mukaone kumene iye amafika, pakuti ndauzidwa kuti ndi wochenjera kwambiri.+
22 Chonde pitani, mukayesetsebe kufufuza kwa aliyense amene anamuonayo, ndipo mukaone kumene iye amafika, pakuti ndauzidwa kuti ndi wochenjera kwambiri.+