2 Tsopano mwamuna wina anali kukhala ku Maoni,+ koma ntchito yake anali kugwirira ku Karimeli.+ Mwamuna ameneyu anali wotchuka kwambiri, ndipo anali ndi nkhosa 3,000 ndi mbuzi 1,000. Tsiku lina, iye anali kugwira ntchito yometa ubweya+ wa nkhosa zake ku Karimeli.