1 Samueli 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amuna amenewa anatichitira zabwino kwambiri, sanativutitse, moti masiku onse amene tinali kuyenda nawo kutchire sitinataye kanthu ngakhale kamodzi.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Tsanzirani, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,7/1/2009, tsa. 19
15 Amuna amenewa anatichitira zabwino kwambiri, sanativutitse, moti masiku onse amene tinali kuyenda nawo kutchire sitinataye kanthu ngakhale kamodzi.+