1 Samueli 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.”
11 Kwa ine, n’zosatheka!+ Sindingachite zimenezi pamaso pa Yehova.+ Sindingatambasule dzanja langa+ ndi kukantha wodzozedwa wa Yehova.+ Choncho, tiye titenge mkondo umene uli chakumutu kwakewo, ndi mtsuko wa madziwo tizipita.”