1 Samueli 28:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”
10 Nthawi yomweyo, Sauli anamulumbirira m’dzina la Yehova kuti: “Pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ sukhala ndi mlandu chifukwa cha nkhani imeneyi!”