2 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”
4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”