-
2 Samueli 2:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Koma Asaheli anakanabe kutembenukira kwina. Choncho Abineri anamubaya* pamimba+ ndi chogwirira cha mkondo, ndipo mkondowo unatulukira kumsana kwake, moti anagwa pansi n’kufera pomwepo. Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, aliyense wofika pamalo amene Asaheli anagwera ndi kufa, anali kuima chilili+ ndi kudabwa kwambiri.
-