2 Samueli 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu.
27 Abineri atabwerera ku Heburoni,+ Yowabu anam’tengera pambali kuchipata kuti alankhulane naye pa awiri.+ Koma kumeneko anamubaya pamimba+ moti anafa chifukwa chokhetsa magazi a Asaheli,+ m’bale wake wa Yowabu.