2 Samueli 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwangondiuza kumene kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka m’tsogolo kwambiri. Limenelitu ndi lamulo limene mwapereka kwa anthu,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+
19 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, kuwonjezeranso pamenepa, mwangondiuza kumene kuti nyumba ya mtumiki wanu idzakhazikika mpaka m’tsogolo kwambiri. Limenelitu ndi lamulo limene mwapereka kwa anthu,+ inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+