2 Samueli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Abisalomu sanalankhule chilichonse, chabwino kapena choipa kwa m’bale wake Aminoni, pakuti Abisalomu anadana+ ndi Aminoni chifukwa chochititsa manyazi Tamara mlongo wake.
22 Abisalomu sanalankhule chilichonse, chabwino kapena choipa kwa m’bale wake Aminoni, pakuti Abisalomu anadana+ ndi Aminoni chifukwa chochititsa manyazi Tamara mlongo wake.