-
2 Samueli 13:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Koma Yehonadabu+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide anati: “Inu mbuyanga musaganize kuti ndi ana onse a mfumu amene aphedwa, pakuti ndi Aminoni yekha amene wafa.+ Abisalomu ndi amene walamula zimenezi kuti zichitike pakuti anakonzeratu+ zimenezi kuyambira pa tsiku limene Aminoniyo anachititsa manyazi+ Tamara mlongo wake.+
-