2 Samueli 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kumeneko kunalinso Zadoki+ pamodzi ndi Alevi+ onse atanyamula+ likasa+ la pangano la Mulungu woona. Choncho Aleviwo anatula pansi likasa la Mulungu woona pafupi ndi Abiyatara+ kufikira anthu onse atamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.
24 Kumeneko kunalinso Zadoki+ pamodzi ndi Alevi+ onse atanyamula+ likasa+ la pangano la Mulungu woona. Choncho Aleviwo anatula pansi likasa la Mulungu woona pafupi ndi Abiyatara+ kufikira anthu onse atamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.