2 Samueli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, ndipo anawoloka Yorodano mpaka m’mawa.+ Onse anawoloka Yorodano popanda wotsala.
22 Nthawi yomweyo Davide ananyamuka pamodzi ndi anthu onse amene anali naye, ndipo anawoloka Yorodano mpaka m’mawa.+ Onse anawoloka Yorodano popanda wotsala.