2 Samueli 19:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “N’chifukwa chiyani+ abale athu a ku Yuda akubweretsani mozemba inu mfumu Davide, pamodzi ndi banja lanu ndi anthu onse amene anali ndi inu kutsidya la Yorodano?”+
41 Pamenepo anthu onse a Isiraeli anabwera kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “N’chifukwa chiyani+ abale athu a ku Yuda akubweretsani mozemba inu mfumu Davide, pamodzi ndi banja lanu ndi anthu onse amene anali ndi inu kutsidya la Yorodano?”+