1 Mafumu 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano ndili ndi pempho limodzi kwa inu. Musandikanire pempho langa.”+ Choncho Bati-seba anamuyankha kuti: “Lankhulani.”
16 Tsopano ndili ndi pempho limodzi kwa inu. Musandikanire pempho langa.”+ Choncho Bati-seba anamuyankha kuti: “Lankhulani.”