1 Mafumu 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+
24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+