1 Mafumu 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo. 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2138-2139, 2244
38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo.