1 Mafumu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nyumbayi inali yosanja kawiri. Nsanjika iliyonse inali ndi mzere wa mawindo. Chotero nyumba yonseyo inali ndi mizere itatu ya mawindo okhala ndi mafelemu. Mawindowo+ anayang’anizana ndi mawindo a mbali ina ya nyumbayo.
4 Nyumbayi inali yosanja kawiri. Nsanjika iliyonse inali ndi mzere wa mawindo. Chotero nyumba yonseyo inali ndi mizere itatu ya mawindo okhala ndi mafelemu. Mawindowo+ anayang’anizana ndi mawindo a mbali ina ya nyumbayo.