1 Mafumu 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Makomo onse a nyumbayo anali ndi mafelemu okhala ndi mbali zonse zinayi zofanana.+ Mbali ya mkati ya windo loyang’anizana ndi windo lina inali ndi felemu lokhala ndi mbali zinayi zofanana. Zinali chonchi mu nsanjika zonse zitatu za nyumbayi.
5 Makomo onse a nyumbayo anali ndi mafelemu okhala ndi mbali zonse zinayi zofanana.+ Mbali ya mkati ya windo loyang’anizana ndi windo lina inali ndi felemu lokhala ndi mbali zinayi zofanana. Zinali chonchi mu nsanjika zonse zitatu za nyumbayi.