1 Mafumu 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mawilowo anawapanga ngati mawilo a galeta.+ Zogwiriziza zake, zingelengele zake, masipokosi ake, ndi mahabu ake, zonse zinali zoumba ndi mkuwa.
33 Mawilowo anawapanga ngati mawilo a galeta.+ Zogwiriziza zake, zingelengele zake, masipokosi ake, ndi mahabu ake, zonse zinali zoumba ndi mkuwa.